Deuteronomo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kumbukirani izi: Simuyenera kuiwala mmene munaputira Yehova Mulungu wanu m’chipululu.+ Anthu inu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova kuyambira tsiku limene munatuluka m’dziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+ Salimo 58:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Oipa akhala opotoka maganizo kuyambira ali m’mimba.+Iwo asochera kuyambira ali m’mimba,Ndipo amalankhula zabodza.+ Salimo 95:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kwa zaka 40, m’badwo umenewo unali kundinyansa,+Ndipo ndinati:“Anthu awa mitima yawo imasochera,+Ndipo sadziwa njira zanga.”+
7 “Kumbukirani izi: Simuyenera kuiwala mmene munaputira Yehova Mulungu wanu m’chipululu.+ Anthu inu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova kuyambira tsiku limene munatuluka m’dziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+
3 Oipa akhala opotoka maganizo kuyambira ali m’mimba.+Iwo asochera kuyambira ali m’mimba,Ndipo amalankhula zabodza.+
10 Kwa zaka 40, m’badwo umenewo unali kundinyansa,+Ndipo ndinati:“Anthu awa mitima yawo imasochera,+Ndipo sadziwa njira zanga.”+