Salimo 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+ Yesaya 48:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Komanso, inu simunafune kumva+ kapena kumvetsa zimenezi. Kuyambira pa nthawi imeneyo kupita m’tsogolo, simunatsegule khutu lanu. Pakuti ine ndinkadziwa ndithu kuti inu munali kuchita zachinyengo,+ ndipo mwatchedwa ‘wochimwa chibadwire.’+
5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+
8 “Komanso, inu simunafune kumva+ kapena kumvetsa zimenezi. Kuyambira pa nthawi imeneyo kupita m’tsogolo, simunatsegule khutu lanu. Pakuti ine ndinkadziwa ndithu kuti inu munali kuchita zachinyengo,+ ndipo mwatchedwa ‘wochimwa chibadwire.’+