Ezekieli 7:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iwo avala ziguduli,*+ ndipo thupi lawo lonse likunjenjemera.+ Pankhope zawo zonse pali manyazi+ ndipo m’mitu yawo yonse muli mipala.+
18 Iwo avala ziguduli,*+ ndipo thupi lawo lonse likunjenjemera.+ Pankhope zawo zonse pali manyazi+ ndipo m’mitu yawo yonse muli mipala.+