Salimo 51:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+ Yeremiya 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Uphunzirepo kanthu pa kuipa kwako+ ndipo zochita zako zosakhulupirika zikudzudzule.+ Dziwa izi, ndipo ona kuti kusiya kwako Yehova Mulungu wako ndi chinthu choipa ndi chowawa.+ Iwe sundiopa ine,’+ watero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.+ Ezekieli 36:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Choncho mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino.+ Mudzanyansidwa ndi zochita zanu, zolakwa zanu ndi zinthu zonyansa zimene munachita.+
4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+
19 Uphunzirepo kanthu pa kuipa kwako+ ndipo zochita zako zosakhulupirika zikudzudzule.+ Dziwa izi, ndipo ona kuti kusiya kwako Yehova Mulungu wako ndi chinthu choipa ndi chowawa.+ Iwe sundiopa ine,’+ watero Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa.+
31 Choncho mudzakumbukira njira zanu zoipa ndi zochita zanu zimene sizinali zabwino.+ Mudzanyansidwa ndi zochita zanu, zolakwa zanu ndi zinthu zonyansa zimene munachita.+