Yesaya 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Maonekedwe a nkhope zawo akuwachitira umboni wotsutsana nawo,+ ndipo anthuwo akunena za tchimo lawo lofanana ndi la Sodomu.+ Iwo sanalibise. Tsoka kwa iwo, chifukwa adzibweretsera mavuto.+ Hoseya 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ ndipo Isiraeli ndi Efuraimu apunthwa ndi zochita zawo.+ Nayenso Yuda wapunthwa pamodzi nawo.+
9 Maonekedwe a nkhope zawo akuwachitira umboni wotsutsana nawo,+ ndipo anthuwo akunena za tchimo lawo lofanana ndi la Sodomu.+ Iwo sanalibise. Tsoka kwa iwo, chifukwa adzibweretsera mavuto.+
5 Kunyada kwa Isiraeli kwakhala umboni womutsutsa,+ ndipo Isiraeli ndi Efuraimu apunthwa ndi zochita zawo.+ Nayenso Yuda wapunthwa pamodzi nawo.+