Hoseya 11:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu anga atsimikiza kuti akhale osakhulupirika kwa ine.+ Akuwaitana kuti abwerere kwa amene ali wokwezeka, koma palibe ngakhale ndi mmodzi yemwe amene akuimirira.
7 Anthu anga atsimikiza kuti akhale osakhulupirika kwa ine.+ Akuwaitana kuti abwerere kwa amene ali wokwezeka, koma palibe ngakhale ndi mmodzi yemwe amene akuimirira.