Salimo 78:57 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 57 Iwo anali kubwerera ndi kuchita zinthu mwachinyengo ngati makolo awo.+Anapotoka maganizo ngati uta wosakunga kwambiri.+ Yeremiya 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova anapitiriza kulankhula nane m’masiku a Mfumu Yosiya kuti:+ “‘Kodi waona zimene Isiraeli wosakhulupirikayu akuchita?+ Akupita kuphiri lililonse lalitali+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira+ kuti akachite uhule kumeneko.+ Yeremiya 8:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 N’chifukwa chiyani anthu a mu Yerusalemu ali osakhulupirika ndipo akhalabe osakhulupirika kwa nthawi yaitali chonchi? Iwo akupitiriza kuchita zachinyengo+ ndipo akana kubwerera.+
57 Iwo anali kubwerera ndi kuchita zinthu mwachinyengo ngati makolo awo.+Anapotoka maganizo ngati uta wosakunga kwambiri.+
6 Yehova anapitiriza kulankhula nane m’masiku a Mfumu Yosiya kuti:+ “‘Kodi waona zimene Isiraeli wosakhulupirikayu akuchita?+ Akupita kuphiri lililonse lalitali+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba ambiri obiriwira+ kuti akachite uhule kumeneko.+
5 N’chifukwa chiyani anthu a mu Yerusalemu ali osakhulupirika ndipo akhalabe osakhulupirika kwa nthawi yaitali chonchi? Iwo akupitiriza kuchita zachinyengo+ ndipo akana kubwerera.+