Hoseya 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Anabwerera, koma sanapite ku chipembedzo choona.+ Anakhala ngati uta wosakungika.+ Akalonga awo adzaphedwa ndi lupanga chifukwa cha mwano wa lilime lawo lomwe.+ N’chifukwa chake iwo adzanyozedwa m’dziko la Iguputo.”+
16 Anabwerera, koma sanapite ku chipembedzo choona.+ Anakhala ngati uta wosakungika.+ Akalonga awo adzaphedwa ndi lupanga chifukwa cha mwano wa lilime lawo lomwe.+ N’chifukwa chake iwo adzanyozedwa m’dziko la Iguputo.”+