Yeremiya 3:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale kuti m’bale wake Yuda amene anali wochita zachinyengoyo anaona zonsezi, iye sanabwerere kwa ine ndi mtima wake wonse+ koma anangobwerera mwachiphamaso,’+ watero Yehova.”
10 Ngakhale kuti m’bale wake Yuda amene anali wochita zachinyengoyo anaona zonsezi, iye sanabwerere kwa ine ndi mtima wake wonse+ koma anangobwerera mwachiphamaso,’+ watero Yehova.”