Salimo 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye adzadula anthu onena kuti: “Ndi lilime lathu tidzapambana.+Timalankhula chilichonse chimene tikufuna ndi milomo yathu. Ndani angatilamulire?” Salimo 73:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kudzikweza kwawo kwafika kumwamba,+Akuyendayenda padziko lapansi ndipo lilime lawo likunena zilizonse zimene akufuna.+ Yesaya 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yerusalemu wapunthwa ndipo Yuda wagwa,+ chifukwa lilime lawo ndiponso zochita zawo n’zotsutsana ndi Yehova.+ Iwo achita zinthu zomupandukira m’maso ake olemekezeka.+
4 Iye adzadula anthu onena kuti: “Ndi lilime lathu tidzapambana.+Timalankhula chilichonse chimene tikufuna ndi milomo yathu. Ndani angatilamulire?”
9 Kudzikweza kwawo kwafika kumwamba,+Akuyendayenda padziko lapansi ndipo lilime lawo likunena zilizonse zimene akufuna.+
8 Yerusalemu wapunthwa ndipo Yuda wagwa,+ chifukwa lilime lawo ndiponso zochita zawo n’zotsutsana ndi Yehova.+ Iwo achita zinthu zomupandukira m’maso ake olemekezeka.+