Ezekieli 36:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo iwo anapita kwa anthu a mitundu ina ndipo anthuwo anayamba kudetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, ndipo anachoka m’dziko lake.’+ Hoseya 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iwe sudzapitiriza kukhala m’dziko la Yehova.+ Efuraimu adzabwerera ku Iguputo+ ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+
20 Pamenepo iwo anapita kwa anthu a mitundu ina ndipo anthuwo anayamba kudetsa dzina langa loyera+ ponena za iwowo kuti, ‘Awa ndi anthu a Yehova, ndipo anachoka m’dziko lake.’+
3 Iwe sudzapitiriza kukhala m’dziko la Yehova.+ Efuraimu adzabwerera ku Iguputo+ ndipo adzadya zinthu zodetsedwa kudziko la Asuri.+