Salimo 119:118 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 118 Onse osochera ndi kuchoka pa malangizo anu mwawataya kutali,+Pakuti ndi achinyengo komanso onama.+ Yeremiya 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Iwe wakhala pakati pa chinyengo.+ Chifukwa cha chinyengo chawo akana kundidziwa ine,”+ watero Yehova.
118 Onse osochera ndi kuchoka pa malangizo anu mwawataya kutali,+Pakuti ndi achinyengo komanso onama.+
6 “Iwe wakhala pakati pa chinyengo.+ Chifukwa cha chinyengo chawo akana kundidziwa ine,”+ watero Yehova.