Miyambo 1:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Popeza ndaitana koma inu mukupitiriza kukana,+ ndatambasula dzanja langa koma palibe amene akumvetsera,+ Hoseya 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+ Aroma 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+ 1 Akorinto 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Dzukani ku tulo tanu+ kuti mukhale olungama ndipo musamachite tchimo, pakuti ena sadziwa Mulungu.+ Ndikulankhula zimenezi kuti muchite manyazi.+
24 Popeza ndaitana koma inu mukupitiriza kukana,+ ndatambasula dzanja langa koma palibe amene akumvetsera,+
6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+
28 Ndiponso monga mmene iwo sanafunire kumudziwa Mulungu molondola,+ iye anawasiya ndi maganizo awo oipa,+ kuti azichita zinthu zosayenerazo,+
34 Dzukani ku tulo tanu+ kuti mukhale olungama ndipo musamachite tchimo, pakuti ena sadziwa Mulungu.+ Ndikulankhula zimenezi kuti muchite manyazi.+