1 Samueli 31:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tsopano Afilisiti anali kumenyana ndi Isiraeli,+ ndipo amuna a Isiraeli anathawa pamaso pa Afilisiti, moti anali kuphedwa+ m’phiri la Giliboa.+ 2 Samueli 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri agwa ndipo afa,+ ngakhalenso Sauli+ ndi mwana wake Yonatani+ afa.”
31 Tsopano Afilisiti anali kumenyana ndi Isiraeli,+ ndipo amuna a Isiraeli anathawa pamaso pa Afilisiti, moti anali kuphedwa+ m’phiri la Giliboa.+
4 Kenako Davide anamufunsa kuti: “Zayenda bwanji kumeneko? Chonde, ndiuze.” Iye anayankha kuti: “Anthu athawa kunkhondo komanso anthu ambiri agwa ndipo afa,+ ngakhalenso Sauli+ ndi mwana wake Yonatani+ afa.”