Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 17:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno Abisalomu anasankha Amasa+ kukhala mtsogoleri wagulu lankhondo kulowa m’malo mwa Yowabu.+ Amasa anali mwana wa munthu wina dzina lake Itara,+ Mwisiraeli amene anagona ndi Abigayeli,+ mwana wamkazi wa Nahasi, mlongo wake wa Zeruya, mayi wake wa Yowabu.

  • 1 Mbiri 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Abigayeli anabereka Amasa,+ ndipo bambo ake a Amasa anali Yeteri+ Mwisimaeli.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena