Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 19:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Amasa mumuuze kuti,+ ‘Kodi iwe sindiwe fupa langa ndi mnofu wanga? Mulungu andilange mowirikiza+ ngati sudzakhala mtsogoleri wa gulu langa lankhondo nthawi zonse m’malo mwa Yowabu.’”+

  • 2 Samueli 20:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Tsopano mfumu inauza Amasa+ kuti: “Ndisonkhanitsire anthu a mu Yuda m’masiku atatu, ndipo iwe uime pano.”

  • 1 Mafumu 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “Iweyo ukudziwa bwino kwambiri zimene Yowabu mwana wa Zeruya anandichita,+ mwa kupha akulu awiri a asilikali a Isiraeli, Abineri+ mwana wa Nera ndi Amasa+ mwana wa Yeteri.+ Mwakutero, anakhetsa magazi+ ankhondo pa nthawi yamtendere. Ndipo anadetsa ndi magazi ankhondo lamba amene anali m’chiuno mwake ndiponso nsapato zimene zinali kuphazi kwake.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena