2 Samueli 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mfumu inauza Amasa kuti:+ “Uitane amuna onse mu Yuda kuti asonkhane kuno pasanathe masiku atatu, ndipo iwenso ubwere.”
4 Mfumu inauza Amasa kuti:+ “Uitane amuna onse mu Yuda kuti asonkhane kuno pasanathe masiku atatu, ndipo iwenso ubwere.”