2 Samueli 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano mfumu inauza Amasa+ kuti: “Ndisonkhanitsire anthu a mu Yuda m’masiku atatu, ndipo iwe uime pano.”
4 Tsopano mfumu inauza Amasa+ kuti: “Ndisonkhanitsire anthu a mu Yuda m’masiku atatu, ndipo iwe uime pano.”