28 Davide atamva zimenezi pambuyo pake, ananena kuti: “Pamaso pa Yehova, ineyo ndi ufumu wanga, mlandu wa magazi+ a Abineri mwana wa Nera sukutikhudza mpaka kalekale.*
31 Mfumuyo inamuuza kuti: “Chita zimene wakuuzazo. Umuphe n’kumuika m’manda ndi kundichotsera ine ndi nyumba ya bambo anga magazi+ amene Yowabu anakhetsa+ popanda chifukwa.