Rute 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kumene inu mudzafere inenso ndidzafera komweko,+ ndipo ndidzaikidwanso komweko. Yehova andilange kwambiri+ ngati chinachake kupatulapo imfa chingandilekanitse ndi inu.” 1 Samueli 3:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ndiyeno Eli anamuuza kuti: “Kodi Mulungu wakuuza chiyani? Chonde usandibisire ayi.+ Mulungu akulange ndi kuwonjezerapo,+ ukandibisira ngakhale mawu amodzi pa mawu onse amene iye wakuuza.”
17 Kumene inu mudzafere inenso ndidzafera komweko,+ ndipo ndidzaikidwanso komweko. Yehova andilange kwambiri+ ngati chinachake kupatulapo imfa chingandilekanitse ndi inu.”
17 Ndiyeno Eli anamuuza kuti: “Kodi Mulungu wakuuza chiyani? Chonde usandibisire ayi.+ Mulungu akulange ndi kuwonjezerapo,+ ukandibisira ngakhale mawu amodzi pa mawu onse amene iye wakuuza.”