1 Mafumu 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mkulu wa asilikali,+ ndipo Zadoki ndi Abiyatara+ anali ansembe. 1 Mbiri 12:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Yehoyada ndiye anali mtsogoleri+ wa ana a Aroni,+ ndipo anali kuyang’anira anthu 3,700.