26 Kwa wansembe Abiyatara,+ mfumuyo inati: “Pita kuminda yako ku Anatoti+ chifukwa ukuyenera kufa.+ Koma lero sindikupha, poti unanyamula likasa la Yehova Ambuye Wamkulu Koposa+ pamaso pa Davide bambo anga,+ ndiponso chifukwa chakuti unavutika nthawi yonse imene bambo anga anavutika.”+