1 Samueli 22:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Koma mwana mmodzi wamwamuna wa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu, dzina lake Abiyatara+ anapulumuka n’kuthawa kutsatira Davide. 1 Mafumu 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Iye anayamba kuchitira zinthu limodzi ndi Yowabu mwana wa Zeruya komanso wansembe Abiyatara.+ Iwowa anayamba kumuthandiza Adoniya+ monga otsatira ake.
20 Koma mwana mmodzi wamwamuna wa Ahimeleki, mwana wa Ahitubu, dzina lake Abiyatara+ anapulumuka n’kuthawa kutsatira Davide.
7 Iye anayamba kuchitira zinthu limodzi ndi Yowabu mwana wa Zeruya komanso wansembe Abiyatara.+ Iwowa anayamba kumuthandiza Adoniya+ monga otsatira ake.