Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Tsopano imva izi, masiku adzafika pamene ndidzadula dzanja lako ndi la nyumba ya kholo lako, moti m’nyumba yako simudzakhala munthu wokalamba.+

  • 1 Samueli 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 (Ahiya ndiye anali kunyamula efodi.+ Iye anali mwana wa Ahitubu,+ m’bale wa Ikabodi,+ mwana wa Pinihasi,+ mwana wa Eli,+ wansembe wa Yehova ku Silo.)+ Koma anthu sanadziwe kuti Yonatani wachoka.

  • 1 Samueli 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, pamene Abiyatara+ mwana wamwamuna wa Ahimeleki anathawira kwa Davide ku Keila, anapita kumeneko atatenga efodi+ m’manja mwake.

  • 1 Samueli 30:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Zitatero, Davide anauza Abiyatara+ wansembe, mwana wa Ahimeleki kuti: “Chonde, bweretsa efodi+ kuno.” Pamenepo Abiyatara anapereka efodi kwa Davide.

  • 2 Samueli 20:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Seva+ anali mlembi,+ ndipo Zadoki+ ndi Abiyatara+ anali ansembe.

  • 1 Mafumu 2:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Choncho Solomo anathamangitsa Abiyatara n’kumusiyitsa kutumikira monga wansembe wa Yehova, pokwaniritsa mawu amene Yehova analankhula ku Silo,+ otsutsana ndi nyumba ya Eli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena