1 Samueli 4:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Iye anatcha mwanayo kuti Ikabodi,*+ n’kunena kuti: “Ulemerero wachoka mu Isiraeli kupita kudziko lina.”+ Ananena zimenezi chifukwa cha likasa la Mulungu woona limene linali litalandidwa, ndiponso chifukwa cha apongozi ake ndi mwamuna wake.+
21 Iye anatcha mwanayo kuti Ikabodi,*+ n’kunena kuti: “Ulemerero wachoka mu Isiraeli kupita kudziko lina.”+ Ananena zimenezi chifukwa cha likasa la Mulungu woona limene linali litalandidwa, ndiponso chifukwa cha apongozi ake ndi mwamuna wake.+