1 Samueli 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 (Ahiya ndiye anali kunyamula efodi.+ Iye anali mwana wa Ahitubu,+ m’bale wa Ikabodi,+ mwana wa Pinihasi,+ mwana wa Eli,+ wansembe wa Yehova ku Silo.)+ Koma anthu sanadziwe kuti Yonatani wachoka.
3 (Ahiya ndiye anali kunyamula efodi.+ Iye anali mwana wa Ahitubu,+ m’bale wa Ikabodi,+ mwana wa Pinihasi,+ mwana wa Eli,+ wansembe wa Yehova ku Silo.)+ Koma anthu sanadziwe kuti Yonatani wachoka.