Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndiyeno zimene zinachitika n’zakuti, pamene Abiyatara+ mwana wamwamuna wa Ahimeleki anathawira kwa Davide ku Keila, anapita kumeneko atatenga efodi+ m’manja mwake.

  • 2 Samueli 15:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kumeneko kunalinso Zadoki+ pamodzi ndi Alevi+ onse atanyamula+ likasa+ la pangano la Mulungu woona. Choncho Aleviwo anatula pansi likasa la Mulungu woona pafupi ndi Abiyatara+ kufikira anthu onse atamaliza kudutsa kuchokera mumzinda.

  • 1 Mbiri 15:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano Davide anawauza kuti: “Inuyo ndinu atsogoleri+ a nyumba ya makolo a Alevi. Choncho inu ndi abale anu mudziyeretse,+ ndipo mukatenge likasa la Yehova Mulungu wa Isiraeli n’kukaliika kumalo amene ine ndakonza kuti likakhaleko.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena