2 Samueli 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara anali ansembe, pamene Seraya anali mlembi. 2 Samueli 20:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Seva+ anali mlembi,+ ndipo Zadoki+ ndi Abiyatara+ anali ansembe. 1 Mafumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya. 1 Mafumu 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Zitatero, mfumu inaika Benaya+ mwana wa Yehoyada m’malo mwa Yowabu kuti akhale mkulu wa asilikali,+ ndipo inaika wansembe Zadoki m’malo mwa Abiyatara.+ 1 Mafumu 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo awa ndiwo akalonga+ amene inali nawo: Wansembe Azariya mwana wa Zadoki,+ 1 Mbiri 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ahitubu anabereka Zadoki,+ Zadoki anabereka Ahimazi,+
17 Zadoki+ mwana wa Ahitubu ndi Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara anali ansembe, pamene Seraya anali mlembi.
8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya.
35 Zitatero, mfumu inaika Benaya+ mwana wa Yehoyada m’malo mwa Yowabu kuti akhale mkulu wa asilikali,+ ndipo inaika wansembe Zadoki m’malo mwa Abiyatara.+