1 Samueli 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Koma iwe khala ndi ine. Usachite mantha. Chifukwa aliyense amene akufunafuna moyo wanga akufunafunanso moyo wako, ndipo ndifunika kukuteteza.”+
23 Koma iwe khala ndi ine. Usachite mantha. Chifukwa aliyense amene akufunafuna moyo wanga akufunafunanso moyo wako, ndipo ndifunika kukuteteza.”+