2 Samueli 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ira Myairi anakhalanso wansembe*+ wa Davide. 1 Mafumu 4:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Azariya mwana wa Natani+ anali mkulu wa nduna, ndipo Zabudu mwana wa Natani anali wansembe, bwenzi+ la mfumu. 1 Mbiri 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti,+ ndipo ana aamuna a Davide ndiwo anali ndi udindo waukulu kwambiri pamaso pa mfumu.+
5 Azariya mwana wa Natani+ anali mkulu wa nduna, ndipo Zabudu mwana wa Natani anali wansembe, bwenzi+ la mfumu.
17 Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti,+ ndipo ana aamuna a Davide ndiwo anali ndi udindo waukulu kwambiri pamaso pa mfumu.+