1 Mafumu 1:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Choncho mfumu inatuma wansembe Zadoki, mneneri Natani, Benaya mwana wa Yehoyada, Akereti ndi Apeleti ndipo iwo anakweza Solomo panyulu yaikazi ya mfumu.+
44 Choncho mfumu inatuma wansembe Zadoki, mneneri Natani, Benaya mwana wa Yehoyada, Akereti ndi Apeleti ndipo iwo anakweza Solomo panyulu yaikazi ya mfumu.+