1 Mafumu 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mfumuyo inawauza kuti: “Tengani atumiki+ a mbuye wanu, n’kukweza Solomo mwana wanga panyulu* yanga yaikazi,+ ndipo mupite naye ku Gihoni.+
33 Mfumuyo inawauza kuti: “Tengani atumiki+ a mbuye wanu, n’kukweza Solomo mwana wanga panyulu* yanga yaikazi,+ ndipo mupite naye ku Gihoni.+