Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 41:43
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 43 Ndiponso, anamukweza pagaleta* lachiwiri laulemu limene anali nalo,+ ndipo anthu anali kufuula patsogolo pake kuti, “A·vrékh!”* posonyeza kuti ndi wamkulu m’dziko lonse la Iguputo.

  • 1 Mafumu 1:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Wansembe Zadoki,+ mneneri Natani,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti+ ndi Apeleti+ anatsetsereka n’kukakweza Solomo panyulu yaikazi ya Mfumu Davide,+ kenako anapita naye ku Gihoni.+

  • Esitere 6:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 amubweretsere zovala zachifumu+ zimene mfumu imavala ndi hatchi* imene mfumu imakwera.+ Hatchiyo aiveke duku lachifumu.

  • Zekariya 9:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 “Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni sangalala kwambiri.+ Fuula mokondwera+ iwe mwana wamkazi wa Yerusalemu. Taona, mfumu yako+ ikubwera kwa iwe.+ Mfumuyo ndi yolungama ndipo yapambana.+ Iyo ndi yodzichepetsa+ ndipo ikubwera itakwera bulu. Ikubwera itakwera nyama yokhwima, imene ndi mwana wamphongo wa bulu.+

  • Luka 19:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Pamenepo iwo anamutenga ndi kupita naye kwa Yesu. Kenako iwo anaponya malaya awo akunja pabuluyo ndi kukwezapo Yesu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena