1 Samueli 30:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndife amene tinakaukira kum’mwera kwa dziko la Akereti+ ndi dera la Yuda komanso kum’mwera kwa dera la Kalebe.+ Ndipo mzinda wa Zikilaga tinautentha ndi moto.” 2 Samueli 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti.+ Ana aamuna a Davide anakhala ansembe.*+
14 Ndife amene tinakaukira kum’mwera kwa dziko la Akereti+ ndi dera la Yuda komanso kum’mwera kwa dera la Kalebe.+ Ndipo mzinda wa Zikilaga tinautentha ndi moto.”
18 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti.+ Ana aamuna a Davide anakhala ansembe.*+