Yoswa 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo Yoswa anadalitsa Kalebe mwana wa Yefune, ndi kum’patsa mzinda wa Heburoni monga cholowa chake.+ Yoswa 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Malo ozungulira mzindawo ndi midzi yake, anawapereka kwa Kalebe mwana wa Yefune kuti akhale ake.+
13 Pamenepo Yoswa anadalitsa Kalebe mwana wa Yefune, ndi kum’patsa mzinda wa Heburoni monga cholowa chake.+