Yoswa 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kalebe+ mwana wa Yefune anam’patsa gawo lake pakati pa ana a Yuda pomvera lamulo la Yehova kwa Yoswa. Anam’patsa Kiriyati-ariba, kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali tate wa Anaki.) Oweruza 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Atapereka Heburoni kwa Kalebe monga mmene Mose analonjezera,+ Kalebe anapitikitsa ana atatu aamuna a Anaki amene anali kukhala mmenemo.+ 1 Mbiri 6:56 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 56 Malo ozungulira mzindawo ndi midzi yake,+ anawapereka kwa Kalebe+ mwana wa Yefune.+
13 Kalebe+ mwana wa Yefune anam’patsa gawo lake pakati pa ana a Yuda pomvera lamulo la Yehova kwa Yoswa. Anam’patsa Kiriyati-ariba, kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali tate wa Anaki.)
20 Atapereka Heburoni kwa Kalebe monga mmene Mose analonjezera,+ Kalebe anapitikitsa ana atatu aamuna a Anaki amene anali kukhala mmenemo.+