Yoswa 15:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kalebe+ mwana wa Yefune anamʼpatsa gawo lake pakati pa ana a Yuda pomvera lamulo la Yehova kwa Yoswa. Anamʼpatsa Kiriyati-ariba, kutanthauza Heburoni. (Ariba anali bambo wa Anaki.)+
13 Kalebe+ mwana wa Yefune anamʼpatsa gawo lake pakati pa ana a Yuda pomvera lamulo la Yehova kwa Yoswa. Anamʼpatsa Kiriyati-ariba, kutanthauza Heburoni. (Ariba anali bambo wa Anaki.)+