Numeri 13:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako Kalebe anayesa kukhazika anthuwo mtima pansi pamaso pa Mose ponena kuti: “Tiyeni tipite pompano, tikatenga dzikolo kukhala lathu, chifukwa tingathe kuwagonjetsa anthuwo.”+ Deuteronomo 1:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune. Iyeyu adzaliona, ndipo ndidzapereka dziko limene anafikako kwa iye ndi ana ake, chifukwa chakuti watsatira Yehova ndi mtima wonse.+
30 Kenako Kalebe anayesa kukhazika anthuwo mtima pansi pamaso pa Mose ponena kuti: “Tiyeni tipite pompano, tikatenga dzikolo kukhala lathu, chifukwa tingathe kuwagonjetsa anthuwo.”+
36 kupatulapo Kalebe mwana wa Yefune. Iyeyu adzaliona, ndipo ndidzapereka dziko limene anafikako kwa iye ndi ana ake, chifukwa chakuti watsatira Yehova ndi mtima wonse.+