Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 10:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Analanda mzindawo ndipo anapha ndi lupanga anthu amene anali mmenemo ndi m’midzi yake yonse, komanso anapha mfumu yawo. Yoswa anaonetsetsa kuti pasakhale wopulumuka. Anachitira mzindawo zonse zimene anachitira mzinda wa Egiloni. Chotero Yoswa anawononga mzindawo ndi aliyense amene anali mmenemo.+

  • Yoswa 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kalebe+ mwana wa Yefune anam’patsa gawo lake pakati pa ana a Yuda pomvera lamulo la Yehova kwa Yoswa. Anam’patsa Kiriyati-ariba, kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali tate wa Anaki.)

  • Yoswa 21:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Anawapatsa Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni.+ (Ariba anali tate wa Anaki.)+ Mzindawu, pamodzi ndi malo ouzungulira odyetserako ziweto, unali m’dera lamapiri la Yuda.+

  • 1 Mbiri 6:56
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 56 Malo ozungulira mzindawo ndi midzi yake,+ anawapereka kwa Kalebe+ mwana wa Yefune.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena