Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 1:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Wansembe Zadoki,+ mneneri Natani,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, Akereti+ ndi Apeleti+ anatsetsereka n’kukakweza Solomo panyulu yaikazi ya Mfumu Davide,+ kenako anapita naye ku Gihoni.+

  • Esitere 6:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo Hamani anatenga chovala+ ndi hatchi, ndipo chovalacho anaveka Moredekai.+ Kenako anam’kwezeka pahatchiyo ndi kumuyendetsa m’bwalo+ la mzinda, akufuula pamaso pake kuti:+ “Umu ndi mmene timachitira ndi munthu amene mfumu yafuna kum’patsa ulemu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena