2 Mbiri 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Hezekiya ndiye anatseka+ kasupe wapamtunda wa madzi+ a ku Gihoni+ ndipo anawapatutsa n’kuwalunjikitsa kumunsi kumadzulo, ku Mzinda wa Davide.+ Ntchito iliyonse imene Hezekiya anali kuchita inali kumuyendera bwino.+
30 Hezekiya ndiye anatseka+ kasupe wapamtunda wa madzi+ a ku Gihoni+ ndipo anawapatutsa n’kuwalunjikitsa kumunsi kumadzulo, ku Mzinda wa Davide.+ Ntchito iliyonse imene Hezekiya anali kuchita inali kumuyendera bwino.+