Yesaya 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Anthu inu mudzaona ming’alu ya Mzinda wa Davide pakuti idzakhala yambiri,+ ndipo mudzatunga madzi a m’dziwe lakumunsi.+ Yesaya 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mudzakumba dziwe pakati pa makoma awiri, losungiramo madzi a dziwe lakale.+ Simudzayang’ana Wolipanga Wamkulu ndipo amene analipanga kalekalelo simudzamuona.
9 Anthu inu mudzaona ming’alu ya Mzinda wa Davide pakuti idzakhala yambiri,+ ndipo mudzatunga madzi a m’dziwe lakumunsi.+
11 Mudzakumba dziwe pakati pa makoma awiri, losungiramo madzi a dziwe lakale.+ Simudzayang’ana Wolipanga Wamkulu ndipo amene analipanga kalekalelo simudzamuona.