Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 20:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Nkhani zina zokhudza Hezekiya ndi zochita zake zonse zamphamvu, ndiponso mmene anakumbira dziwe+ ndi ngalande+ n’kubweretsa madzi mumzindawo, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.

  • 2 Mbiri 32:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Hezekiya ndiye anatseka+ kasupe wapamtunda wa madzi+ a ku Gihoni+ ndipo anawapatutsa n’kuwalunjikitsa kumunsi kumadzulo, ku Mzinda wa Davide.+ Ntchito iliyonse imene Hezekiya anali kuchita inali kumuyendera bwino.+

  • Nehemiya 3:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Saluni mwana wamwamuna wa Kolihoze, kalonga wa chigawo cha Mizipa,+ anakonza Chipata cha Kukasupe.+ Iye anachimanga ndi kukhoma denga* lake. Anaikanso zitseko zake,+ akapichi ake ndi mipiringidzo yake. Iye anamanganso mpanda wa Dziwe+ la Ngalande* kukafika ku Munda wa Mfumu+ ndi ku Masitepe+ ochokera ku Mzinda wa Davide.+

  • Yohane 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kenako anamuuza kuti: “Pita ukasambe+ m’dziwe la Siloamu”+ (dzina limene kumasulira kwake ndi ‘Otumidwa’). Choncho anapita kukasamba,+ ndipo anabwerako akuona.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena