Yohane 9:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye anayankha kuti: “Munthu wina dzina lake Yesu anakanda thope ndi kupaka m’maso mwangamu, ndiyeno anandiuza kuti, ‘Pita ku Siloamu+ ukasambe.’ Ndinapitadi kukasamba ndipo ndayamba kuona.”
11 Iye anayankha kuti: “Munthu wina dzina lake Yesu anakanda thope ndi kupaka m’maso mwangamu, ndiyeno anandiuza kuti, ‘Pita ku Siloamu+ ukasambe.’ Ndinapitadi kukasamba ndipo ndayamba kuona.”