Yohane 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kenako anamuuza kuti: “Pita ukasambe+ m’dziwe la Siloamu”+ (dzina limene kumasulira kwake ndi ‘Otumidwa’). Choncho anapita kukasamba,+ ndipo anabwerako akuona.+
7 Kenako anamuuza kuti: “Pita ukasambe+ m’dziwe la Siloamu”+ (dzina limene kumasulira kwake ndi ‘Otumidwa’). Choncho anapita kukasamba,+ ndipo anabwerako akuona.+