1 Mafumu 1:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mfumuyo inawauza kuti: “Tengani atumiki+ a mbuye wanu, n’kukweza Solomo mwana wanga panyulu* yanga yaikazi,+ ndipo mupite naye ku Gihoni.+ 1 Mafumu 1:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ndiyeno wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akamudzoza ku Gihoni kukhala mfumu.+ Kenako abwerako akusangalala ndipo m’mudzimo muli phokoso lokhalokha. Phokoso limenelo ndi limene munamva lija.+
33 Mfumuyo inawauza kuti: “Tengani atumiki+ a mbuye wanu, n’kukweza Solomo mwana wanga panyulu* yanga yaikazi,+ ndipo mupite naye ku Gihoni.+
45 Ndiyeno wansembe Zadoki ndi mneneri Natani akamudzoza ku Gihoni kukhala mfumu.+ Kenako abwerako akusangalala ndipo m’mudzimo muli phokoso lokhalokha. Phokoso limenelo ndi limene munamva lija.+