2 Samueli 20:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno Davide anauza Abisai+ kuti: “Tsopano Sheba+ mwana wamwamuna wa Bikiri atisautsa kwambiri kuposa Abisalomu.+ Iweyo utenge atumiki+ a mbuye wako ndi kumuthamangitsa kuti asapeze mizinda ya mipanda yolimba kwambiri ndi kutizemba ife tikuona.”
6 Ndiyeno Davide anauza Abisai+ kuti: “Tsopano Sheba+ mwana wamwamuna wa Bikiri atisautsa kwambiri kuposa Abisalomu.+ Iweyo utenge atumiki+ a mbuye wako ndi kumuthamangitsa kuti asapeze mizinda ya mipanda yolimba kwambiri ndi kutizemba ife tikuona.”