2 Mbiri 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Hezekiya ndiye anatseka+ kasupe wapamtunda wa madzi+ a ku Gihoni+ ndipo anawapatutsa n’kuwalunjikitsa kumunsi kumadzulo, ku Mzinda wa Davide.+ Ntchito iliyonse imene Hezekiya anali kuchita inali kumuyendera bwino.+ Yesaya 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Tsopano Yehova anauza Yesaya kuti: “Pita ukakumane ndi Ahazi. Upite ndi mwana wako Seari-yasubu.*+ Ukakumane ndi Ahaziyo pamapeto pa ngalande+ yochokera kudziwe lakumtunda, m’mphepete mwa msewu waukulu wopita kumalo a wochapa zovala.+
30 Hezekiya ndiye anatseka+ kasupe wapamtunda wa madzi+ a ku Gihoni+ ndipo anawapatutsa n’kuwalunjikitsa kumunsi kumadzulo, ku Mzinda wa Davide.+ Ntchito iliyonse imene Hezekiya anali kuchita inali kumuyendera bwino.+
3 Tsopano Yehova anauza Yesaya kuti: “Pita ukakumane ndi Ahazi. Upite ndi mwana wako Seari-yasubu.*+ Ukakumane ndi Ahaziyo pamapeto pa ngalande+ yochokera kudziwe lakumtunda, m’mphepete mwa msewu waukulu wopita kumalo a wochapa zovala.+