Yesaya 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zozizwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa makamu amene amakhala m’phiri la Ziyoni.+
18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zozizwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa makamu amene amakhala m’phiri la Ziyoni.+