Yesaya 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mwanayo asanafike podziwa kukana choipa ndi kusankha chabwino,+ nthaka ya mafumu awiri amene ukuchita nawo mantha ofika podwala nawowo, idzakhala itasiyidwiratu.+ Yesaya 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako ndinakhala malo amodzi ndi mneneri wamkazi ndipo iye anatenga pakati. Pambuyo pake anabereka mwana wamwamuna.+ Tsopano Yehova anandiuza kuti: “Um’patse dzina lakuti Maheri-salala-hasi-bazi, Aheberi 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Komanso pamene akunena kuti: “Ndidzadalira iye.”+ Ndi kutinso: “Taonani! Ine ndi ana amene Yehova anandipatsa.”+
16 Mwanayo asanafike podziwa kukana choipa ndi kusankha chabwino,+ nthaka ya mafumu awiri amene ukuchita nawo mantha ofika podwala nawowo, idzakhala itasiyidwiratu.+
3 Kenako ndinakhala malo amodzi ndi mneneri wamkazi ndipo iye anatenga pakati. Pambuyo pake anabereka mwana wamwamuna.+ Tsopano Yehova anandiuza kuti: “Um’patse dzina lakuti Maheri-salala-hasi-bazi,
13 Komanso pamene akunena kuti: “Ndidzadalira iye.”+ Ndi kutinso: “Taonani! Ine ndi ana amene Yehova anandipatsa.”+